Ekisodo 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Farao atafika pafupi, Aisiraeli anakweza maso awo ndipo anaona Aiguputo akuwathamangira. Choncho Aisiraeli anachita mantha kwambiri ndipo anayamba kufuulira Yehova.+
10 Farao atafika pafupi, Aisiraeli anakweza maso awo ndipo anaona Aiguputo akuwathamangira. Choncho Aisiraeli anachita mantha kwambiri ndipo anayamba kufuulira Yehova.+