Ekisodo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi zimene tinkakuuza ku Iguputo kuja si zimenezi? Kodi sitinakuuze kuti, ‘Tisiye tizitumikira Aiguputoʼ? Chifukwa ndi bwino kuti tizitumikira Aiguputo kusiyana nʼkuti tifere mʼchipululu.”+
12 Kodi zimene tinkakuuza ku Iguputo kuja si zimenezi? Kodi sitinakuuze kuti, ‘Tisiye tizitumikira Aiguputoʼ? Chifukwa ndi bwino kuti tizitumikira Aiguputo kusiyana nʼkuti tifere mʼchipululu.”+