Ekisodo 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzalemekeza dzina langa pogonjetsa Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.”+
18 Ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzalemekeza dzina langa pogonjetsa Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.”+