Ekisodo 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtambowo unaima pakati pa Aiguputo ndi Aisiraeli.+ Mbali imodzi unkachititsa mdima, ndipo mbali ina unkawaunikira usiku.+ Choncho gulu la Aiguputo silinayandikire gulu la Aisiraeli usiku wonse.
20 Mtambowo unaima pakati pa Aiguputo ndi Aisiraeli.+ Mbali imodzi unkachititsa mdima, ndipo mbali ina unkawaunikira usiku.+ Choncho gulu la Aiguputo silinayandikire gulu la Aisiraeli usiku wonse.