Ekisodo 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno chakumʼbandakucha,* Yehova ali mʼchipilala cha mtambo ndi cha moto chija,+ anayangʼana gulu la Aiguputo ndipo anachititsa kuti Aiguputowo asokonezeke.
24 Ndiyeno chakumʼbandakucha,* Yehova ali mʼchipilala cha mtambo ndi cha moto chija,+ anayangʼana gulu la Aiguputo ndipo anachititsa kuti Aiguputowo asokonezeke.