Ekisodo 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye ankagulula mawilo a magaleta awo moti ankawayendetsa movutikira. Ndipo Aiguputo ankanena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+
25 Iye ankagulula mawilo a magaleta awo moti ankawayendetsa movutikira. Ndipo Aiguputo ankanena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+