-
Ekisodo 14:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako nʼkuloza panyanja kuti madzi abwerere nʼkumiza Aiguputo, magaleta awo ankhondo ndi asilikali awo apamahatchi.”
-