Ekisodo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Madzi amene anabwererawo anamiza magaleta ankhondo, asilikali apamahatchi ndi gulu lonse lankhondo la Farao, amene analondola Aisiraeli mʼnyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+
28 Madzi amene anabwererawo anamiza magaleta ankhondo, asilikali apamahatchi ndi gulu lonse lankhondo la Farao, amene analondola Aisiraeli mʼnyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+