Ekisodo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aisiraeli anaonanso mphamvu* zazikulu zimene Yehova anagwiritsa ntchito pogonjetsa Aiguputo. Ndipo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+
31 Aisiraeli anaonanso mphamvu* zazikulu zimene Yehova anagwiritsa ntchito pogonjetsa Aiguputo. Ndipo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+