Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Nsanja ya Olonda,10/15/1995, ptsa. 10-117/1/1990, ptsa. 18-19
2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+