Ekisodo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mafunde amphamvu awakwirira. Amira pansi pa nyanja ngati mwala.+