Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati: ‘Ndiwathamangira nʼkuwapeza! Ndigawa chuma chawo mpaka nditakhutira! Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
9 Mdaniyo anati: ‘Ndiwathamangira nʼkuwapeza! Ndigawa chuma chawo mpaka nditakhutira! Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+