Ekisodo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munasonyeza chikondi chanu chokhulupirika potsogolera anthu amene munawawombola.+Ndi mphamvu zanu, mudzawatsogolera kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:13 Yandikirani, tsa. 285
13 Munasonyeza chikondi chanu chokhulupirika potsogolera anthu amene munawawombola.+Ndi mphamvu zanu, mudzawatsogolera kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.