Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzanjenjemera.Anthu okhala ku Filisitiya adzamva ululu.*