Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+