Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+