Ekisodo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mahatchi a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa mʼnyanja,+Yehova wabweza madzi amʼnyanjamo nʼkuwamiza.+Koma Aisiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+
19 Mahatchi a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa mʼnyanja,+Yehova wabweza madzi amʼnyanjamo nʼkuwamiza.+Koma Aisiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+