Ekisodo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamene amuna ankaimba, Miriamu ankathirira mangʼombe kuti: “Imbirani Yehova chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.”+
21 Pamene amuna ankaimba, Miriamu ankathirira mangʼombe kuti: “Imbirani Yehova chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.”+