Ekisodo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo anafika ku Mara,+ koma sanathe kumwa madzi a ku Mara chifukwa anali owawa. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Mara.*
23 Iwo anafika ku Mara,+ koma sanathe kumwa madzi a ku Mara chifukwa anali owawa. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Mara.*