-
Ekisodo 15:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Iye anawauza kuti: “Mukadzamvera ndi mtima wonse mawu a Yehova Mulungu wanu, nʼkuchita zinthu zoyenera pamaso pake ndiponso kumvera malamulo ake ndi kusunga malangizo ake onse,+ sindidzakugwetserani matenda aliwonse amene ndinagwetsera Aiguputo,+ chifukwa ine Yehova ndi amene ndikukuchiritsani.”+
-