-
Ekisodo 15:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kenako anafika ku Elimu kumene kunali akasupe 12 a madzi ndi mitengo 70 ya kanjedza. Choncho iwo anamanga msasa pamenepo pafupi ndi madzi.
-