Ekisodo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aisiraeliwo ankauza Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera mʼdziko la Iguputo, kumene tinkadya nyama+ ndi mkate nʼkukhuta. Mʼmalomwake mwatibweretsa mʼchipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 153/15/1993, tsa. 21
3 Aisiraeliwo ankauza Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera mʼdziko la Iguputo, kumene tinkadya nyama+ ndi mkate nʼkukhuta. Mʼmalomwake mwatibweretsa mʼchipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+