-
Ekisodo 16:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mawa mʼmawa mudzaona ulemerero wa Yehova chifukwa wamva kungʼungʼudza kwanu kotsutsana ndi Yehovayo. Ife ndi ndani kuti muzitingʼungʼudzira?”
-