Ekisodo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Mose anauza Aroni kuti: “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Bwerani pamaso pa Yehova, chifukwa wamva kungʼungʼudza kwanu.’”+
9 Choncho Mose anauza Aroni kuti: “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Bwerani pamaso pa Yehova, chifukwa wamva kungʼungʼudza kwanu.’”+