Ekisodo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mame aja atauma, panthaka yamʼchipululumo panapezeka tinthu topyapyala ndi tolimba koma tosalala+ ngati madzi amene aundana panthaka.
14 Mame aja atauma, panthaka yamʼchipululumo panapezeka tinthu topyapyala ndi tolimba koma tosalala+ ngati madzi amene aundana panthaka.