Ekisodo 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova walamula kuti, ‘Aliyense atole chakudya chimenechi mogwirizana ndi mmene amadyera. Munthu aliyense muzimutolera muyezo wa omeri*+ imodzi mogwirizana ndi chiwerengero cha anthu amene ali mutenti yanu.’”
16 Yehova walamula kuti, ‘Aliyense atole chakudya chimenechi mogwirizana ndi mmene amadyera. Munthu aliyense muzimutolera muyezo wa omeri*+ imodzi mogwirizana ndi chiwerengero cha anthu amene ali mutenti yanu.’”