-
Ekisodo 16:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma iwo sanamvere Mose. Anthu ena atasiya chakudyacho mpaka mʼmawa, chinatuluka mphutsi nʼkuyamba kununkha, moti Mose anawakalipira kwambiri.
-