Ekisodo 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo iye anawayankha kuti: “Ndi zimene Yehova wanena. Mawa ndi tsiku lopuma,* ndi sabata lopatulika la Yehova.+ Zimene mungaphike, phikani, ndipo zimene mungawiritse, wiritsani.+ Zotsala zonse muziike pambali nʼkuzisunga mpaka mʼmawa.”
23 Ndipo iye anawayankha kuti: “Ndi zimene Yehova wanena. Mawa ndi tsiku lopuma,* ndi sabata lopatulika la Yehova.+ Zimene mungaphike, phikani, ndipo zimene mungawiritse, wiritsani.+ Zotsala zonse muziike pambali nʼkuzisunga mpaka mʼmawa.”