Ekisodo 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:29 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 162/15/1993, tsa. 27
29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.”