Ekisodo 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:34 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 31
34 Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.