Ekisodo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi anthu ake Aisiraeli komanso mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+
18 Ndiyeno Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi anthu ake Aisiraeli komanso mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+