Ekisodo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anatenganso ana aamuna awiri a Zipora.+ Mwana wina, Mose anamupatsa dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”
3 Anatenganso ana aamuna awiri a Zipora.+ Mwana wina, Mose anamupatsa dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”