Ekisodo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwana winayo anamupatsa dzina lakuti Eliezere,* ndipo anati: “Mulungu wa atate anga ndi amene amandithandiza, chifukwa anandipulumutsa kwa Farao amene ankafuna kundipha.”+
4 Mwana winayo anamupatsa dzina lakuti Eliezere,* ndipo anati: “Mulungu wa atate anga ndi amene amandithandiza, chifukwa anandipulumutsa kwa Farao amene ankafuna kundipha.”+