Ekisodo 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mose anafotokozera apongozi akewo zonse zimene Yehova anachitira Farao ndi Iguputo pofuna kuthandiza Isiraeli.+ Anawafotokozera mavuto onse amene anakumana nawo mʼnjira+ komanso mmene Yehova anawapulumutsira.
8 Mose anafotokozera apongozi akewo zonse zimene Yehova anachitira Farao ndi Iguputo pofuna kuthandiza Isiraeli.+ Anawafotokozera mavuto onse amene anakumana nawo mʼnjira+ komanso mmene Yehova anawapulumutsira.