-
Ekisodo 18:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno Yetero anati: “Yehova atamandike, amene anakupulumutsani ku Iguputo ndiponso kwa Farao, amenenso analanditsa anthuwa kwa Aiguputo omwe ankawazunza.
-