-
Ekisodo 18:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako Yetero, apongozi ake a Mose, anabweretsa nsembe yopsereza ndi nsembe zina kwa Mulungu. Ndipo Aroni ndi akulu onse a Isiraeli anabwera nʼkudyera limodzi chakudya ndi apongozi ake a Mose, pamaso pa Mulungu woona.
-