-
Ekisodo 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Apongozi a Mose ataona zonse zimene iye ankachitira anthuwo anati: “Kodi anthuwa ukuchita nawo chiyani? Nʼchifukwa chiyani wangokhala wekha ndipo anthu onsewa aima pamaso pako kuyambira mʼmawa mpaka madzulo?”
-