Ekisodo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano mvera zimene ndikufuna kukuuza. Ndikupatsa malangizo ndipo Mulungu adzakhala nawe.+ Iweyo uzilankhula ndi Mulungu woona mʼmalo mwa anthuwa+ komanso uzipititsa milandu kwa Mulungu woona.+
19 Tsopano mvera zimene ndikufuna kukuuza. Ndikupatsa malangizo ndipo Mulungu adzakhala nawe.+ Iweyo uzilankhula ndi Mulungu woona mʼmalo mwa anthuwa+ komanso uzipititsa milandu kwa Mulungu woona.+