Ekisodo 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho iwo ankaweruza anthuwo pakakhala mlandu. Mlandu wovuta ankapita nawo kwa Mose,+ koma mlandu uliwonse waungʼono ankauweruza.
26 Choncho iwo ankaweruza anthuwo pakakhala mlandu. Mlandu wovuta ankapita nawo kwa Mose,+ koma mlandu uliwonse waungʼono ankauweruza.