Ekisodo 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ananyamuka ku Refidimu+ nʼkulowa mʼchipululu cha Sinai ndipo anamanga msasa wawo mʼchipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+
2 Ananyamuka ku Refidimu+ nʼkulowa mʼchipululu cha Sinai ndipo anamanga msasa wawo mʼchipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+