Ekisodo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose anakwera mʼphirimo kukaonekera kwa Mulungu woona.+ Ndipo Yehova analankhula naye mʼphirimo kuti: “Ukanene mawu awa kunyumba ya Yakobo kapena kuti kwa Aisiraeli,
3 Kenako Mose anakwera mʼphirimo kukaonekera kwa Mulungu woona.+ Ndipo Yehova analankhula naye mʼphirimo kuti: “Ukanene mawu awa kunyumba ya Yakobo kapena kuti kwa Aisiraeli,