Ekisodo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mose anatsika ndipo anaitanitsa akulu onse a anthu nʼkuwauza mawu onse amene Yehova anamulamula.+
7 Choncho Mose anatsika ndipo anaitanitsa akulu onse a anthu nʼkuwauza mawu onse amene Yehova anamulamula.+