Ekisodo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Yehova anafika pamwamba pa phiri la Sinai. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo ndipo Mose anakweradi.+
20 Choncho Yehova anafika pamwamba pa phiri la Sinai. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo ndipo Mose anakweradi.+