Ekisodo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera kuti akuyeseni+ nʼcholinga choti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+
20 Ndiyeno Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera kuti akuyeseni+ nʼcholinga choti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+