Ekisodo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukagula kapolo wa Chiheberi,+ adzakhala kapolo wanu kwa zaka 6, koma mʼchaka cha 7 muzimumasula ndipo azichoka osapereka chilichonse.+
2 Mukagula kapolo wa Chiheberi,+ adzakhala kapolo wanu kwa zaka 6, koma mʼchaka cha 7 muzimumasula ndipo azichoka osapereka chilichonse.+