Ekisodo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati sanamuphe mwadala ndipo Mulungu woona walola kuti zichitike, ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+
13 Koma ngati sanamuphe mwadala ndipo Mulungu woona walola kuti zichitike, ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+