Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu akamupsera mtima mnzake mpaka kumupha mwadala,+ munthuyo aziphedwa. Ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe, muzimuchotsa nʼkukamupha.+
14 Munthu akamupsera mtima mnzake mpaka kumupha mwadala,+ munthuyo aziphedwa. Ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe, muzimuchotsa nʼkukamupha.+