Ekisodo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Munthu akaba ngʼombe kapena nkhosa nʼkuipha kapena kuigulitsa, azilipira ngʼombe 5 pa ngʼombe imodzi imene waba, ndi nkhosa 4 pa nkhosa imodzi imene waba.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:1 Nsanja ya Olonda,6/15/1992, tsa. 30
22 “Munthu akaba ngʼombe kapena nkhosa nʼkuipha kapena kuigulitsa, azilipira ngʼombe 5 pa ngʼombe imodzi imene waba, ndi nkhosa 4 pa nkhosa imodzi imene waba.+