-
Ekisodo 22:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma ngati zachitika dzuwa litatuluka, amene wamuphayo ali ndi mlandu wa magazi.)
Wakuba azilipira ndipo ngati alibe kalikonse, azigulitsidwa kuti alipire zinthu zimene anabazo.
-