-
Ekisodo 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ngati munthu waika ziweto zake kuti zidye mʼmunda wa mpesa kapena wa mbewu zina, ndipo wazilekerera kuti zikadye mʼmunda wa munthu wina, azilipira popereka zokolola zabwino koposa zamʼmunda wake wa mpesa kapena zamʼmunda wake wa mbewu zina.
-